Judges 1:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Ayuda adathira nkhondo mzinda wa Yerusalemu, naulanda. Adapha anthu ambiri, natentha mzinda wonsewo ndi moto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a Yuda anachita nkhondo pa Yerusalemu, naulanda, naukantha ndi lupanga lakuthwa, natentha mudzi ndi moto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pambuyo pake Ayuda anakathira nkhondo mzinda wa Yerusalemu ndipo anawulanda. Anapha anthu ambiri ndi kutentha mzinda wonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a Yuda anacita nkhondo pa Yerusalemu, naulanda, naukantha ndi lupanga lakuthwa, natentha mudzi ndi moto.