Judges 10:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adafunsa Aisraele kuti, “Kodi suja Ine ndidakupulumutsani kwa Aejipito, Aamori, Aamoni ndi Afilisti?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anati kwa ana a Israele, Kodi sindinakupulumutsani kwa Aejipito ndi kwa Aamori, ndi kwa ana a Amoni, ndi kwa Afilisti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anawafunsa kuti, “Suja ine ndinakupulumutsani kwa Aigupto, Aamori, Aamoni ndi Afilisti?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anati kwa ana a Israyeli, Kodi sindinakupulumutsani kwa Aaigupto ndi kwa Aamori, ndi kwa ana a Amoni, ndi kwa Aftlisti?