Judges 10:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Asidoni, Aamaleke ndi Amaoni, adaakusautsani, inu nkundilirira kuti ndikuthandizeni, suja Ine ndidakupulumutsani kwa anthu amene aja?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Asidoni omwe, ndi Aamaleke, ndi Amaoni anakupsinjani. Pamenepo munafuula kwa Ine, ndipo ndinakupulumutsani m'dzanja lao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndiponso pamene Asidoni, Aamaleki ndi Amoni anakuzunzani, inu nʼkulirira kwa ine suja ndinakupulumutsani kwa anthu amenewa?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Asidoni omwe, ndi Aamaleki, ndi Amidyani anakupsinjani. Pamenepo munapfuula kwa Ine, ndipo ndinakupulumutsani m'dzanja lao.