Judges 10:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe Ine mwandisiya, mukutumikira milungu ina. Nchifukwa chake sindidzakupulumutsaninso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mwandisiya Ine ndi kutumikira milungu ina, chifukwa chake sindikupulumutsaninso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe inu mwandikana ndipo mukutumikira milungu ina. Choncho sindidzakupulumutsaninso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mwandisiya Ine ndi kutumikira milungu yina, cifukwa cace sindikupulumutsaninso.