Judges 10:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho adachotsa milungu yachilendo pakati pao nayamba kutumikira Chauta, ndipo Chauta adamva chisoni poona Aisraele akuzunzika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anachotsa milungu yachilendo pakati pao, natumikira Yehova; ndipo mtima wake unagwidwa chisoni chifukwa cha mavuto a Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anachotsa milungu ya chilendo pakati pawo ndi kuyamba kutumikira Yehova. Ndipo Yehova anamva chisoni poona mmene Aisraeli ankazunzikira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anacotsa milungu yacilendo pakati pao, natumikira Yehova; ndipo mtima wace unagwidwa cisoni cifukwa ca mabvuto a Israyeli.