Judges 10:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atafa Tola padabwera Yairo Mgiliyadi amene adaweruza Aisraele zaka 22.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atafa iye, anauka Yairi Mgiliyadi, naweruza Israele zaka makumi awiri mphambu ziwiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atafa Tola panabwera Yairi wa ku Giliyadi, amene anatsogolera Israeli kwa zaka 22.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atafa iye, anauka Yairi Mgileadi, naweruza Israyeli zaka makumi awiri mphambu ziwiri.