Judges 11:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yefita wa ku Giliyadi anali wankhondo wamphamvu. Bambo wake anali Giliyadi, mai wake anali mkazi wadama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yefita Mgiliyadi ndipo anali ngwazi yamphamvu, ndiye mwana wa mkazi wadama; koma Giliyadi adabala Yefita.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yefita wa ku Giliyadi anali wankhondo wa mphamvu. Iyeyu amayi ake anali mkazi wachiwerewere, ndipo abambo ake anali Giliyadi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yefita Mgileadi ndipo anali ngwazi yamphamvu, ndiye mwana wa mkazi wadama; koma Gileadi adabala Yefita.