Judges 11:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akuluakulu a ku Giliyadi aja adamuuza Yefita kuti, “Chabwino, tikuvomera zimene ukunenazi, Chauta ndiye mboni yathu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo akulu a Giliyadi anati kwa Yefita, Yehova ndiye wakumvera pakati pa ife, tikapanda kuchita monga momwe wanena.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akuluakulu a ku Giliyadi anamuyankha kuti, “Yehova akhale mboni pakati pa inu ndi ife, ngati sitidzachita monga mwa mawu anu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo akuru a Gileadi anati kwa Yefita, Yehova ndiye wakumvera pakati pa ife, tikapanda kucita monga momwe wanena.