Judges 11:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Yefita adatuma amithenga kwa mfumu ya Aamoni kukanena kuti, “Kodi ine ndakulakwirani chiyani kuti muzimenyana nkhondo ndi dziko langa?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yefita anatuma mithenga kwa mfumu ya ana a Amoni, ndi kuti, Ndi chiyani ndi inu ndi kuti mwandidzera kuthira nkhondo dziko langa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Yefita anatuma amithenga kwa mfumu ya Aamoni ndi funso lakuti, “Kodi ife takuchimwirani chiyani kuti muzichita nkhondo ndi dziko langa?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yefita anatuma mithenga kwa mfumu ya ana a Amoni, ndi kuti, Ndi ciani ndi Inu, ndi kuti Mwandidzera kuthira nkhondo dziko langa?