Judges 11:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yefita adatumanso amithenga kwa mfumu ya Aamoni,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yefita anatumanso mithenga kwa mfumu ya ana a Amoni;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yefita anatumizanso amithenga akewo kwa mfumu ya Aamoni
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yefita anatumanso mithenga kwa mfumu ya ana a Amoni;