Judges 11:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kukanena kuti, “Yefita akuti: Aisraele sadalande dziko la Amowabu kapenanso dziko la Aamoni ai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nanena naye, Atero Yefita, Israele sanalande dziko la Mowabu kapena dziko la ana a Amoni;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kukanena kuti, Yefita akuti, “Israeli sanalande dziko la Mowabu kapena dziko la Aamoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nanena naye, Atero Yefita, Israyeli sanalanda dziko la Moabu kapena dziko la ana a Amoni;