Judges 11:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiponso kodi inuyo mukupambana Balaki, mwana wa Zipori, mfumu ya ku Mowabu? Kodi iye uja adaaputanapo ndi Aisraele kapena kumenyana nawo nkhondo?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsopano kodi inu ndinu wabwino woposa Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu; anatengana konse ndi Israele iyeyu kodi, kapena kuchita nao nkhondo konse kodi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ndinu abwino kuposa Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu? Kodi iye anakanganapo kapena kuchita nkhondo ndi Israeli?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsopano kodi inu ndinu wabwino woposa Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Moabu; anatengana konse ndi Israyeli iyeyu kodi, kapena kucita nao nkhondo konse kodi?