Judges 11:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Yefita adaoloka kunka kwa Aamoni kukamenyana nawo nkhondo. Ndipo Chauta adamthandiza kuŵagonjetsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero Yefita anapita kwa ana a Amoni kuwathira nkhondo; ndipo Yehova anawapereka m'dzanja lake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Yefita anawolokera kwa Aamoni kukamenya nawo nkhondo, ndipo Yehova anawaperekadi mʼmanja mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero Yefita anapita kwa ana a Amoni kuwathira nkhondo; ndipo Yehova anawapereka m'dzanja lace;