Judges 11:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwanayo adayankha kuti, “Atate, ngati mwalonjeza Chauta ndi pakamwa panu, chiteni zimene mwalonjeza, pakuti tsopano Chauta wakuthandizani kulipsira Aamoni, adani anu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati kwa iye, Atate wanga, mwamtegulira Yehova pakamwa panu, mundichitire ine monga umo mudatulutsa mau pakamwa panu; popeza Yehova anakuchitirani inu chilango pa adani anu, pa ana a Amoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwanayo anayankha kuti, “Abambo, ngati munalonjeza kwa Yehova ndi pakamwa panu, chitani zimene munalonjezera pakuti Yehova wakuthandizani kulipsira adani anu Amowabu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati kwa iye, Atate wanga, mwamtsegulira Yehova pakamwa panu, mundicitire ine monga umo mudaturutsa mau pakamwa panu; popeza Yehova anakucitirani inu cilango pa adani anu, pa ana a Amoni.