Judges 11:39 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Miyezi iŵiriyo itatha, adabwerera kwa bambo wake ndipo adamchita monga momwe adaalonjezera. Namwaliyo anali asanadziŵe mwamuna. Motero chidasanduka chizoloŵezi m'dziko la Aisraele,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali pakutha miyezi iwiri, anabwerera kwa atate wake amene anamchitira monga mwa chowinda chake anachiwinda; ndipo sanamdziwe mwamuna. Motero unali mwambo m'Israele,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Miyezi iwiri itatha iye anabwerera kwa abambo ake, ndipo anachitadi zimene analonjeza. Motero unakhala mwambo wa Aisraeli,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali pakutha miyezi iwiri, anabwerera kwa atate wace amene anamcitira monga mwa cowinda cace anaciwinda; ndipo sanamdziwa mwamuna. Motero unali mwambo m'Israyeli,