Judges 11:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti ana aakazi a ku Israele ankapita chaka ndi chaka kukalira maliro a mwana wa Yefita Mgiliyadi uja, masiku anai pa chaka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti ana akazi a Israele akamuka chaka ndi chaka kumliririra mwana wa Yefita wa ku Giliyadi, masiku anai pa chaka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti atsikana a Israeli ankapita chaka chilichonse kukalira maliro a mwana wa mkazi wa Yefita, Mgiliyadi uja masiku makumi anayi pa chaka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti ana akazi a Israyeli akamuka caka ndi caka kumliririra mwana wa Yefita wa ku Gileadi, masiku anai pa caka.