Judges 11:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yefita adaŵauza akuluakulu a ku Giliyadiwo kuti, “Mukandibwezeranso kwathu kuti ndikamenye nkhondo ndi Aamoni, ndipo Chauta akandithandiza kuŵagonjetsa, ndidzakhaladi wokulamulirani.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yefita anati kwa akulu a Giliyadi, Mukandifikitsanso kwathu kuchita nkhondo ndi ana a Amoni, nakawapereka Yehova pamaso panga, ndidzakhala mkulu wanu kodi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yefita anawayankha akuluakulu a ku Giliyadi kuti, “Ngati mundibwezeranso kwathu kuti ndikachite nkhondo ndi Aamoni ndipo Yehova nʼkukandithandiza kuwagonjetsa, ndidzakhaladi wokulamulirani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yefita anati kwa akuru a Gileadi, Mukaodifikitsanso kwathu kucita nkhondo ndi ana a Amoni, nakawapereka Yehova pamaso panga, ndidzakhala mkuru wanu kodi?