Judges 12:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yefita adaŵauza kuti, “Ine ndi anthu anga tidaakangana kwambiri ndi Aamoni. Ndidakuitanani, koma inu simudadzandipulumutse kwa iwowo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yefita anati kwa iwo, Ine ndi anthu anga tinatsutsana kwakukulu ndi ana a Amoni, koma pamene ndinakuitanani inu simunandipulumutsa m'dzanja lao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yefita anayankha kuti, “Ine ndi anthu anga tinakangana kwambiri ndi Aamoni. Ndinakuyitanani koma inu simunandipulumutse mʼmanja mwawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yefita anati kwa iwo, Ine ndi anthu anga tinatsutsana kwakukuru ndi ana a Amoni, koma pamene ndinakuitanani inu simunandipulumutsa m'dzanju lao.