Judges 13:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aisraele adachimwiranso Chauta. Ndipo Chauta adaŵapereka m'manja mwa Afilisti pa zaka makumi anai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a Israele anaonjeza kuchita choipa pamaso pa Yehova; nawapereka Yehova m'dzanja la Afilisti zaka makumi anai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aisraeli anachitanso zinthu zoyipira Yehova, kotero Yehova anawapereka mʼmanja mwa Afilisti kwa zaka makumi anayi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a Israyeli anaonjeza kucita coipa pamaso pa Yehova; nawapereka Yehova m'dzanja la Afilisti zaka makumi anai.