Judges 13:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkazi uja adathamanga nakauza mwamuna wake kuti, “Munthu uja adaabwera kuno tsiku lijaliyu wandiwonekeranso.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mkaziyo anafulumira nathamanga, nauza mwamuna wake, nanena naye, Taona, wandionekera munthu anandidzerayo tsiku lija.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono mkaziyo anathamanga kukawuza mwamuna wake kuti, “Wandionekeranso munthu uja amene anabwera kwa ine tsiku lija.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mkaziyo anafulumira nathamanga, nauza mwamuna wace, nanena naye, Taona, wandionekera munthu anandidzerayo tsiku lija.