Judges 13:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Manowa adanyamuka natsata mkazi wake, ndipo adakafika kumene kunali munthuyo nakamufunsa kuti, “Kodi inu ndinu amene mudaalankhula ndi amaiŵa?” Iye adayankha kuti, “Inde ndinedi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nanyamuka Manowa natsata mkazi wake, namdzera mwamuna uja, nanena naye, Kodi ndinu mwamuna uja munalankhula ndi mkaziyu? Ndipo anati, Ndine amene.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Manowa ananyamuka namutsatira mkazi wake. Atafika kwa munthuyo anamufunsa kuti, “Kodi ndinu munayankhula ndi mkazi wanga?” Iye anayankha kuti, “Ndine.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nanyamuka Manowa natsata mkazi wace, namdzera mwamuna uja, nanena naye, Kodi ndinu mwamuna ujamunalankhulandimkaziyu? Ndipo anati, Ndine amene.