Judges 13:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Manowa adamufunsa kuti, “Tsono zimene mudanenazi zikadzachitikadi, kodi mnyamatayo azidzakhala bwanji, ndipo azidzachita chiyani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati Manowa, Achitike tsopano mau anu; koma makhalidwe ake a mwanayo ndi machitidwe ake adzatani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Manowa anafunsa kuti, “Tiyerekeze kuti mawu anuwa akwaniritsidwadi, ndiye mwanayu azidzakhala bwanji ndipo azidzachita chiyani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati Manowa, Acitike tsopano mau anu; koma makhalidwe ace a mwanayo ndi macitidwe ace adzatani?