Judges 13:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Manowa adauza mngelo wa Chauta kuti, “Pepani, tayambani mwaima, tikuti tikuwotchereni kamwanakambuzi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Manowa anati kwa mthenga wa Yehova, Tiloleni tikuchedwetseni kuti tikukonzereni mwanawambuzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Manowa anamuwuza mngelo wa Yehova uja kuti, “Chonde dikirani pangʼono, timati tikukonzereni mwana wambuzi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Manowa anati kwa mthenga wa Yehova, Tiloleni tikucedwetseni kuti tikukonzereni mwana wa mbuzi.