Judges 13:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Manowa adauza mngeloyo kuti, “Timati mutiwuze dzina lanu kuti tidzakulemekezeni, zikadzachitikadi zimene mwanenazi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Manowa anati kwa mthenga wa Yehova, Dzina lanu ndani, kuti, atachitika mau anu, tikuchitireni ulemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Manowa anapempha mngelo wa Yehova kuti, “Chonde tidziwitseni dzina lanu kuti zikadzachitika zimene mwanenazi ife tidzakulemekezeni?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Manowa anati kwa mthenga wa Yehova, Dzina lanu ndani, kuti, atacitika mau anu, tikucitireni ulemu.