Judges 13:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ku Zora kunali munthu wina, wa fuko la Dani, dzina lake Manowa. Mkazi wake analibe ana, anali wosabereka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali munthu wina wa Zora wa banja la Adani, dzina lake ndiye Manowa; ndi mkazi wake analibe mwana, sanabala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ku Zora kunali munthu wina dzina lake Manowa, wochokera ku fuko la Dani. Mkazi wake analibe ana popeza anali wosabereka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali munthu wina wa Zora wa banja la Adani, dzina lace ndiye Manowa; ndi mkazi wace analibe mwana, sanabala.