Judges 13:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adauza mkazi wake kuti, “Ife ndiye tifatu basi, nanga sitaona Mulungu!”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati Manowa kwa mkazi wake, Tidzafa ndithu pakuti taona Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anawuza mkazi wake kuti, “Ife tifa basi pakuti taona Mulungu!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati Manowa kwa mkazi wace, Tidzafa ndithu pakuti taona Mulungu.