Judges 14:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Samisoni adapita ku Timna ndipo kumeneko adaonako mtsikana wachifilisti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Samisoni anatsikira ku Timna, naona mkazi wa ku Timna wa ana akazi a Afilisti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Samsoni anapita ku Timna ndipo kumeneko anaonako mtsikana wa Chifilisiti.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Samsoni anatsikira ku Timna, naona mkazi wa ku Timna wa ana akazi a Afilisti.