Judges 14:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bambo wakeyo adapita kunyumba kwa mkazi uja, ndipo Samisoni adakonza phwando kumeneko, pakuti ndi m'mene ankachitira anyamata.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo atate wake anatsikira kwa mkazi; ndi Samisoni anakonzerapo madyerero; pakuti amatero anyamata.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano Samsoni anapita ku nyumba kwa mtsikanayo. Ndipo kumeneko Samsoni anakonza phwando monga ankachitira anyamata.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo atate wace anatsikira kwa mkazi; ndi Samsoni anakonzerapo madyerero; pakuti amatero anyamata.