Judges 14:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene anthu adamuwona, adabwera ndi anyamata makumi atatu kuti akhale naye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, pamene anamuona, anabwera nao anzake makumi atatu akhale naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Makolo a mkwatibwiyo atamuona, anasankha anyamata makumi atatu kuti akhale naye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, pamene anamuona, anabwera nao anzace makumi atatu akhale naye.