Judges 14:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mukalephera kundiwuza tanthauzo lake, mudzandipatsa ndinu zovala zabafuta makumi atatu, ndiponso zovala za tsiku lachikondwerero makumi atatu.” Iwo adamuyankha kuti, “Tiphere mwambiwo, tiwumve.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma ngati simukhoza kunditanthauzira uwu mudzandipatsa ndinu malaya a nsalu yabafuta makumi atatu ndi zovala zosinthanitsa makumi atatu. Pamenepo ananena naye, Mwambi wako tiumve.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati simutha kundiwuza tanthauzo lake, inuyo mudzandipatsa zovala makumi atatu zabafuta ndi zina za tsiku la chikondwerero.” Iwo anamuyankha kuti, “Tiwuze mwambi wakowo tiwumve.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma ngati simukhoza kunditanthauzira uwu mudzandipatsa ndinu Malaya a nsaru yabafuta makumi atatu ndi zobvala zosinthanitsa makumi atatu. Pamenepo ananena naye, Mwambi wako tiumve.