Judges 14:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atabwerera kwao adakauza bambo ndi mai wake kuti, “Ku Timna ndaonako mtsikana wachifilisti. Mukanditengere ameneyo, ndidzamkwatire.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nakwera iye, nauza atate wake ndi amai wake, nati, Ndapenya mkazi m'Timna wa ana akazi a Afilisti; ndipo tsono munditengere uyu akhale mkazi wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atabwerera kwawo, anawuza abambo ndi amayi ake kuti, “Ine ndaona mtsikana wa Chifilisiti ku Timna, tsono mukanditengere ameneyo kuti akhale mkazi wanga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nakwera iye, nauzaatatewacendi amai wace, nati, Ndapenya mkazi m'Timna wa ana akazi a Afilisti; ndipo tsono munditengere uyu akhale mkazi wanga.