Judges 14:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi yomweyo mkazi wa Samisoni uja bambo wake adamkwatitsa kwa mnzake wa Samisoniyo amene adaali mnzake womuperekeza paukwati paja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mkazi wake wa Samisoni anakhala wa mnzake, amene adakhala bwenzi lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mkazi wa Samsoniyo anamukwatitsa kwa amene anali mnzake womuperekeza pa ukwati paja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mkazi wace wa Samsoni anakhala wa mnzace, amene adakhala bwenzi lace.