Judges 14:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Patapita kanthaŵi Samisoni adabwerera kudzamtenga mtsikanayo. Pa njira adapatuka kukaona mkango adaaupha uja. Adangoona njuchi zili mu mkangowo pamodzi ndi uchi wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atapita masiku ndipo anabweranso kudzamtenga, napatuka iye kukaona mtembo wa mkango; ndipo taona, m'chitanda cha mkango munali njuchi zoundana, ndi uchi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Patapita nthawi, Samsoni anabwerera kukatenga mtsikana uja. Panjira anapatuka kukaona mkango unawupha uja, ndipo anangoona njuchi zili mu mkangowo pamodzi ndi uchi wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atapita masiku ndipo anabweranso kudzamtenga, napambuka iye kukaona mtembo wa mkango; ndipo taona, m'citanda ca mkango munali njuci zoundana, ndi uci.