Judges 15:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake, adachitaya pansi chibwano chija, ndipo malowo adatchedwa Ramatilehi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, atatha kunena, anataya chibwano m'dzanja lake; nawatcha malowo Ramatilehi ndiko kunena chitunda cha chibwano.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atatsiriza kuyankhula, anataya chibwanocho, ndipo malowo anawatcha Ramati-Lehi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, atatha kunena, anataya cibwano m'dzanja lace; nawacha maiowo Ramati-leki ndiko kunena citunda ca cibwano.