Judges 15:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Samisoni adakagwira nkhandwe mazana atatu nazimangirira michira ziŵiriziŵiri. Kenaka pa mfundo iliyonse ya michirayo adamangirirapo nsakali naziyatsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Namuka Samisoni, nagwira ankhandwe mazana atatu, natenga miuni, nalunza michira, naika muuni pakati pa michira iwiri iliyonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Samsoni anapita nakagwira nkhandwe 300 nazimangirira michira ziwiriziwiri ndipo pa fundo iliyonse ya michirayo anamangirira nsakali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Namuka Samsoni, nagwira ankhandwe mazana atatu, natenga miuni, nalunza micira, naika muuni pakati pa micira iwiri iri yonse.