Judges 15:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atamva zimenezi Samisoni adati, “Ngati zimenezi nzimene mumachita, ndikulumbira kuti sindileka mpaka nditakulipsirani.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Samisoni ananena nao, Mukatero ndidzakubwezerani chilango ndi pamenepo ndidzaleka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Samsoni anawawuza kuti, “Ngati mumachita zangati zimenezi, ndiye ine sindileka mpaka nditakulipsirani.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Samsoni ananena nao, Mukatero ndidzakubwezerani cilango ndi pamenepo ndidzaleka.