Judges 16:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Samisoni adapita ku Gaza ndipo kumeneko adaonako mkazi wadama naloŵa m'nyumba yake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Samisoni anamuka ku Gaza, naonako mkazi wadama, nalowana naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku lina Samsoni anapita ku Gaza. Kumeneko anaonako mkazi wachiwerewere, ndipo analowa mu nyumba yake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Samsoni anamuka ku Gaza, naonako mkazi wadama, nalowana naye.