Judges 16:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Samisoni adauza mkaziyo kuti, “Atandimanga ndi zingwe zatsopano zimene sadazigwiritse ntchito, ndidzasanduka wofooka, ndipo ndidzafanafana ndi munthu wina aliyense.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nanena naye, Akandimangitsa nazo zingwe zatsopano, zosagwira nazo ntchito pamenepo ndidzakhala wofooka wakunga munthu wina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anati, “Ngati aliyense atandimanga ine ndi zingwe zatsopano zimene sanazigwiritseko ntchito, ndidzasanduka wofowoka ndi kukhala monga munthu wina aliyense.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nanena naye, Akandimangitsa nazo zingwe zatsopano, zosagwira nazo nchito pamenepo ndidzakhala: wofoka wakunga munthu wina.