Judges 16:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Samisoni adauza mnyamata amene adamgwira dzanja kuti, “Undilole ndikhudze mizati imene yachirikiza nyumba yonseyi, kuti ndiitsamire.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Samisoni anati kwa mnyamata womgwira dzanja, Ndileke, ndikhudze mizati imene nyumba ikhazikikapo, kuti nditsamirepo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pambuyo pake Samsoni anawuza mnyamata amene anamugwira dzanja kuti, “Ndilole kuti ndikhudze mizati imene yachirikiza nyumba yonseyi kuti ndiyitsamire.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Samsoni anati kwa mnyamata womgwira dzanja, Ndileke, ndikhudze mizati imene nyumba ikhazikikapo, kuti nditsamirepo.