Judges 16:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pomwepo Samisoni adagwira mizati iŵiri yapakati imene inkachirikiza nyumbayo. Adaitsamira ndi mphamvu zake zonse, dzanja lake lamanja lili pa mzati wina, lamanzere lili pa mzati winanso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Samisoni anagwira mizati iwiri ya pakati imene nyumba inakhazikikapo, natsamirapo wina ndi dzanja lamanja, ndi unzake ndi dzanja lamanzere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Samsoni anagwira mizati iwiri yapakati imene inkachirikiza nyumbayo. Anayitsamira ndi mphamvu zake zonse, dzanja lake lamanja ku mzati wina ndi dzanja lamanzere ku mzati winanso,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Samsoni anagwira mizati iwiri ya pakati imene nyumba inakhazikikapo, natsamirapo wina ndi dzanja lamanja, ndi unzace ndi dzanja lamanzere.