Judges 16:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Samisoni adayamba kukonda mkazi wina wa ku chigwa cha Soreki, dzina lake Delila.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pambuyo pake kunali kuti anakonda mkazi m'chigwa cha Soreki, dzina lake ndiye Delila.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pambuyo pake, Samsoni anayamba kukonda mtsikana wina wa ku chigwa cha Soreki dzina lake Delila.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pambuyo pace kunali kud anakonda mkazi m'cigwa ca Soreki, dzina lace ndiye Delila.