Judges 16:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Samisoni adamuuza kuti, “Atandimanga ndi nsinga zatsopano zisanu ndi ziŵiri zosauma, ndidzasanduka wofooka ndipo ndidzafanafana ndi munthu wina aliyense.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nanena naye Samisoni, Akandimanga nazo nsinga zatsopano zisanu ndi ziwiri zosauma, ndidzakhala wofooka, wakunga munthu wina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Samsoni anamuyankha kuti, “Ngati wina atandimanga ndi zingwe zisanu ndi ziwiri zatsopano zosawuma, ndidzafowoka ndi kusanduka ngati munthu wina aliyense.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nanena naye Samsoni, Akandimanga nazo nsinga zatsopano zisanu ndi ziwiri zosauma, ndidzakhala wofoka, wakunga munthu wina.