Judges 17:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mleviyo adavomera kukhala naye munthuyo, ndipo adasanduka ngati mmodzi mwa ana ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Mleviyo anavomera kukhalitsa ndi munthuyo; ndi mnyamatayo anamkhalira ngati mmodzi wa ana ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Mleviyo anavomera kuti azikhala naye, ndipo mnyamatayo anakhala ngati mmodzi mwa ana ake aamuna.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Mleviyo anabvomera kukhalitsa ndi munthuyo; ndi mnyamatayo anamkhalira ngati mmodzi wa ana ace.