Judges 17:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Mika adati, “Tsopano ndikudziŵa kuti Chauta adzandilemeza, popeza kuti Mleviyu ndiye wansembe wanga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati Mika, Tsopano ndidziwa kuti Yehova adzandichitira chokoma, popeza ndili naye Mlevi akhale wansembe wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Mika anati, “Tsopano ndadziwa kuti Yehova adzandikomera mtima chifukwa Mleviyu ndiye wakhala wansembe wanga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati Mika, Tsopano ndidziwa kuti Yehova adzandicitira cokoma, popeza ndiri naye Mlevi akhale wansembe wanga.