Judges 17:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono iye adabwezera ndalama zonse kwa mai wake, ndipo maiyo pofuna kuchotsa temberero lija, adati, “Ndikuzipatula ndalama zasilivazi kuti zikhale za Chauta. Ndidzazipereka kuti aseme fano ndi kulikuta ndi siliva. Choncho ndikubwezera ndalamazo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nabwezera amake ndalama zija mazana khumi ndi limodzi; nati amai wake, Kupatula ndapatulira Yehova ndalamazo zichoke ku dzanja langa, zimuke kwa mwana wanga, kupanga nazo fano losema ndi fano loyenga; m'mwemo ndikubwezera izi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Mika anabweza ndalama 1,100 za siliva kwa amayi ake, ndipo amayi akewo anati, “Ine ndapatulira Yehova ndalama za silivazi kuti mwana wanga aseme fano ndi kulikuta ndi siliva. Ndiye tsopano ndikubwezera ndalamazo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nabwezera amace ndarama zija mazana khumi ndi limodzi; nati amai wace, Kupatula ndapatulira Yehova ndaramazo zicoke ku dzanja langa, zimuke kwa mwana wanga, kupanga nazo dikupempha fano losema ndi fane loyenga; m'mwemo ndikubwezera izi.