Judges 17:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mika uja adamufunsa kuti, “Kodi inu kwanu nkuti?” Munthuyo adayankha kuti, “Ine ndine Mlevi wa ku Betelehemu m'dziko la Yuda, ndikufunafuna koti ndikhale nao.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mika ananena naye, Ufumira kuti? Nati kwa iye, Ndine Mlevi wa ku Betelehemu-Yuda, ndilikumuka kugonera kumene ndikapeza pokhala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Mika anamufunsa kuti, “Mukuchokera kuti?” Ndipo iye anayakha kuti, “Ndine Mlevi wochokera ku Betelehemu mʼdziko la Yuda. Ndikufunafuna malo okhala.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mika ananena naye, Ufumira kuti? Nati kwa iye, Ndine Mlevi wa ku Betelehemu-Yuda, ndirikumuka kugonera kumene ndikapeza pokhala.