Judges 18:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukapita, mukaŵapeza kuti ndi anthu opanda tcheru. Dzikolo nlalikulu. Ndithudi Mulungu walipereka m'manja mwanu dziko limenelo. Malowo ngosasoŵa kanthu kalikonse kopezeka pa dziko lapansi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pomuka inu mudzafikira anthu okhazikika mtima ndi dziko lachitando; pakuti Mulungu walipereka m'dzanja lanu; pamenepo mposasowa kanthu kalikonse kali pa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mukalowa, mukapeza anthu amene ali osatekeseka ndi dziko lalikulu. Yehova wakupatsani dziko limeneli. Malowo ngosasowa kanthu kalikonse kopezeka pa dziko lapansi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pomuka inu mudzafikira anthu okhazikika mtima ndi dziko ladtando; pakuti Mulungu walipereka m'dzanja lanu; pamenepo mposasowa kanthu kali konse kali pa dziko lapansi.