Judges 18:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuchokera kumeneko adapita ku dziko lamapiri la ku Efuremu, nakafika ku nyumba ya Mika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapitirira komweko kunka ku mapiri a Efuremu, nadza kunyumba ya Mika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuchokera kumeneko anapita ku dziko lamapiri la Efereimu ndipo anafika ku nyumba ya Mika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapiririra komweko kumka ku mapiri a Efraimu, nadza ku nyumba ya Mika.