Judges 18:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi imeneyo nkuti anthu 600 a fuko la Dani okhala ndi zida zankhondo aja ataima pa khomo lapachipata.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo amuna mazana asanu ndi limodzi omangira zida zao za nkhondo m'chuuno, ndiwo a ana a Dani, analikuima polowera pa chipata;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawi imeneyi nʼkuti anthu 600 a fuko la Dani aja atayima pa chipata atanyamula zida za nkhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo amuna mazana asanu ndi limodzi omangira zida zao za nkhondo m'cuuno, ndiwo a ana a-Dani, analikuima polowera pa cipata;