Judges 18:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwowo adafuulira anthu a fuko la Dani aja ndipo anthu a fuko la Daniwo adatembenukira kumbuyo nafunsa Mika kuti, “Kodi chakuvuta nchiyani kuti uzibwera ndi chigulu chotere?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anafuula kwa ana a Dani. Nacheuka iwo nati kwa Mika, Chakusowa chiyani, kuti wamemeza anthu ako?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atawafuwulira, a fuko la Dani aja anachewuka ndipo anafunsa Mika kuti, “Chavuta nʼchiyani kuti usonkhanitse anthu chotere?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapfuula kwa ana a Dani. Naceuka iwo nati kwa Mika, Cakusowa ciani, kuti wamemeza anthu ako?